"Mutu" เนื้อเพลง
"Mutu" มีเนื้อเพลงในภาษา ภาษาอังกฤษ
"Mutu" ความหมายมาจากภาษา ภาษาอังกฤษ และไม่ได้แปลงเป็นภาษาอังกฤษในปัจจุบัน
A film by Kulair
Stream #digitalmaskini here :
Mutu
Zandpweteka zili Mmutu
Mutu
Sikut ndangofasa ndikudya Mutu
Nyimbo za Vuta muma Hood
ma babe Thako boys kugwedezera mutu
Sindikupanga za Munthu
Koma sindiopa munthu
Adani asandidwalitse Mutu
Ndufuna Mkazi wa bho andipase Mutu
Kwacha ku chaser Ku Kachaso Ngati Mutu
Bottle mmanja Blunt pakamwa Chifukwa Zili Mutu
ika Nyimbo za abale ngati ukupanga connect Bluetooth
Usalenge sumafira Takuona Ukugwedeza mutu
Ukamaphweketsa Titha kukusosola Ngati Nkhuku
Tikuvaya Chapter ina Ngati kikuwelenga buku
ngati ine ndi a’
è tili bhobho
Ndizabhobho
Palibe wina andi uze ndiku Mova slow
Ngati Ii show ya Probonal Usataye Nthawi Ndikundiimbira phone
I get the bag n I’m Gone
Ndimakonda ku ku Hasa chifukwa maluzi samva Chisoni
Osandi Halla Sukuona Ndili mu Zone
Sindimangoshala man ndima pusher Mission
Zot ndiwe dolo eeeh zimandigiligisha #music